Yohane 6:16 - Buku Lopatulika Koma pofika madzulo, ophunzira ake anatsikira kunyanja; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Koma pofika madzulo, ophunzira ake anatsikira kunyanja; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa M'mene kunkayamba kuda, ophunzira ake a Yesu adatsikira ku nyanja. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Pofika madzulo, ophunzira ake anatsikira ku nyanja, |
ndipo pamene adalowa m'ngalawa, analikuoloka nyanja kunka ku Kapernao. Ndipo kutada pamenepo, koma Yesu asanadze kwa iwo.