Yohane 5:47 - Buku Lopatulika Koma ngati simukhulupirira malembo a iyeyu, mudzakhulupirira bwanji mau anga? Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Koma ngati simukhulupirira malembo a iyeyu, mudzakhulupirira bwanji mau anga? Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Koma ngati simukhulupirira zimene iyeyo adalemba, nanga mungakhulupirire bwanji mau anga?” Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Koma ngati simukhulupirira zimene iye analemba, mudzakhulupirira bwanji zimene Ine ndikunena?” |
Koma anati kwa iye, Ngati samvera Mose ndi aneneri, sadzakopeka mtima ngakhale wina akauka kwa akufa.
ndi kuti kuyambira ukhanda wako wadziwa malembo opatulika, okhoza kukupatsa nzeru kufikira chipulumutso, mwa chikhulupiriro cha mwa Khristu Yesu.