Ndipo ine ndine wozunzika ndi waumphawi; koma Ambuye andikumbukira ine. Inu ndinu mthandizi wanga, ndi Mpulumutsi wanga, musamachedwa, Mulungu wanga.
Yohane 4:49 - Buku Lopatulika Mkuluyo ananena kwa Iye, Ambuye, tsikani asanafe mwana wanga. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Mkuluyo ananena kwa Iye, Ambuye, tsikani asanafe mwana wanga. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Ndunayo idati, “Ndapota nanu Ambuye, tiyeni mwana wanga asanafe.” Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Nduna ya mfumuyo inati, “Ambuye tiyeni mwana wanga asanafe.” |
Ndipo ine ndine wozunzika ndi waumphawi; koma Ambuye andikumbukira ine. Inu ndinu mthandizi wanga, ndi Mpulumutsi wanga, musamachedwa, Mulungu wanga.
nanena, kuti, Kamwana kanga kabuthu kalinkutsirizika; ndikupemphani Inu mufikeko, muike manja anu pa iko, kuti kapulumuke, ndi kukhala ndi moyo.
Pamenepo Yesu anati kwa iye, Ngati simuona zizindikiro ndi zozizwa, simudzakhulupirira.
Yesu ananena naye, Muka, mwana wako ali ndi moyo. Munthuyo anakhulupirira mau amene Yesu anatero naye, namuka.