Pamenepo Pilato, m'mene adamva mau awa, anatuluka ndi Yesu, nakhala pansi pa mpando woweruzira kumalo dzina lake, Bwalo lamiyala, koma mu Chihebri, Gabata.
Yohane 19:8 - Buku Lopatulika Ndipo pamene Pilato anamva mau awa, anaopa koposa. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo pamene Pilato anamva mau awa, anaopa koposa. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Pamene Pilato adamva mau ameneŵa, adachita mantha kwabasi. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Pilato atamva zimenezi, anachita mantha kwambiri, |
Pamenepo Pilato, m'mene adamva mau awa, anatuluka ndi Yesu, nakhala pansi pa mpando woweruzira kumalo dzina lake, Bwalo lamiyala, koma mu Chihebri, Gabata.
Ayuda anamyankha iye, Tili nacho chilamulo ife, ndipo monga mwa chilamulocho ayenera kufa, chifukwa anadziyesera Mwana wa Mulungu.
Ndipo analowanso ku Pretorio, nanena kwa Yesu, Muchoka kuti? Koma Yesu sanamyankhe kanthu.