Yohane 18:6 - Buku Lopatulika Ndipo m'mene anati kwa iwo, Ndine, anabwerera m'mbuyo, nagwa pansi. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo m'mene anati kwa iwo, Ndine, anabwerera m'mbuyo, nagwa pansi. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Pamene Yesu adaŵayankha kuti, “Ndine, ndilipo,” iwo adabwerera m'mbuyo nagwa pansi. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Pamene Yesu anati, “Ndine,” iwo anabwerera mʼmbuyo ndi kugwa pansi. |
Pondifika ine ochita zoipa kudzadya mnofu wanga, inde akundisautsa ndi adani anga, anakhumudwa iwo nagwa.
Achite manyazi nadodome iwo akulondola moyo wanga kuti auononge. Abwerere m'mbuyo, nachite manyazi iwo okondwera kundichitira choipa.
Anayankha Iye, Yesu Mnazarayo. Yesu ananena nao, Ndine. Koma Yudasi yemwe, wompereka Iye, anaima nao pamodzi.