Ine ndawapatsa iwo mau anu; ndipo dziko lapansi, linadana nao, chifukwa sakhala a dziko lapansi, monga Ine sindikhala wa dziko lapansi.
Yohane 17:16 - Buku Lopatulika Siali a dziko lapansi monga Ine sindili wa dziko lapansi. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Siali a dziko lapansi monga Ine sindili wa dziko lapansi. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Iwo sali a dziko lapansi, monga Inenso sindili wa dziko lapansi. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Iwo si a dziko lapansi, monga Ine sindilinso wa dziko lapansi. |
Ine ndawapatsa iwo mau anu; ndipo dziko lapansi, linadana nao, chifukwa sakhala a dziko lapansi, monga Ine sindikhala wa dziko lapansi.
Ndipo ananena nao, Inu ndinu ochokera pansi; Ine ndine wochokera Kumwamba; inu ndinu a dziko lino lapansi; sindili Ine wa dziko lino lapansi.