Ndipo pamene ananyamuka pakupemphera anadza kwa ophunzira, nawapeza ali m'tulo ndi chisoni,
Yohane 16:6 - Buku Lopatulika Koma chifukwa ndalankhula izi ndi inu chisoni chadzala mumtima mwanu. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Koma chifukwa ndalankhula izi ndi inu chisoni chadzala mumtima mwanu. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa M'mitima mwanu mwadzaza chisoni chifukwa ndakuuzani zimenezi. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Muli ndi chisoni kwambiri chifukwa ndakuwuzani zimene. |
Ndipo pamene ananyamuka pakupemphera anadza kwa ophunzira, nawapeza ali m'tulo ndi chisoni,
Ndipo anati kwa iwo, Mau awa ndi otani mulandizanawo poyendayenda? Ndipo anaima ndi nkhope zao zachisoni.