Pamenepo mfumu Ahasuwero inalankhula, niti kwa mkazi wamkulu Estere, Ndani uyu, ali kuti iyeyu wadzazidwa mtima wake kuti azitero?
Yohane 13:25 - Buku Lopatulika Iyeyu potsamira pomwepo, pa chifukwa cha Yesu, anena ndi Iye, Ambuye, ndiye yani? Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Iyeyu potsamira pomwepo, pa chifukwa cha Yesu, anena ndi Iye, Ambuye, ndiye yani? Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Pamenepo iyeyo adatsamira pachifukwa pa Yesu, namufunsa kuti, “Ambuye, mukunena yani kodi?” Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Atamutsamiranso Yesuyo, anamufunsa Iye kuti, “Ambuye, kodi ndani?” |
Pamenepo mfumu Ahasuwero inalankhula, niti kwa mkazi wamkulu Estere, Ndani uyu, ali kuti iyeyu wadzazidwa mtima wake kuti azitero?
Petro, m'mene anacheuka, anapenya wophunzira amene Yesu anamkonda alikutsata, amenenso anatsamira pachifuwa pake pamgonero, nati, Ambuye, ndani iye wakupereka Inu?