Ndipo Abrahamu anatcha dzina lake la malowo Yehova-Yire: monga ati lero lomwe, M'phiri la Yehova chidzaoneka.
Yohane 11:6 - Buku Lopatulika Chifukwa chake pamene anamva kuti anadwala, anakhala pamenepo pamalo pomwepo masiku awiri. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Chifukwa chake pamene anamva kuti anadwala, anakhala pamenepo pa malo pomwepo masiku awiri. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Komabe pamene adamva za matendawo, Yesu adaswera masiku aŵiri pamalo pomwe adaaliripo. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Koma atamva kuti Lazaro akudwala, Iye anakhalabe kumene anali masiku ena awiri. |
Ndipo Abrahamu anatcha dzina lake la malowo Yehova-Yire: monga ati lero lomwe, M'phiri la Yehova chidzaoneka.
Ndipo anawafotokozera iwo nalira, nawatembenukiranso, nanena nao, nampatula Simeoni mwa iwo, nammanga iye pamaso pao.
Chifukwa chake Yehova adzadikira, kuti akukomereni mtima, ndipo chifukwa chake Iye adzakuzidwa, kuti akuchitireni inu chifundo; pakuti Yehova ndiye Mulungu wa chiweruziro; odala ali onse amene amdikira Iye.