Pamenepo Marita, pakumva kuti Yesu alinkudza, anamuka kukakomana ndi Iye; koma Maria anakhalabe m'nyumba.
Yohane 11:30 - Buku Lopatulika (Koma Yesu sanafike kumudzi, koma anali pamalo pomwe Marita adakomana ndi Iye.) Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 (Koma Yesu sanafike kumudzi, koma anali pamalo pomwe Marita adakomana ndi Iye.) Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Pamenepo nkuti Yesu asanafike kumudziko, koma anali chikhalire pamalo pomwe Marita adaakumana naye. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Tsopano nʼkuti Yesu asanalowe mʼmudzi, koma anali akanali pa malo pamene Marita anakumana naye. |
Pamenepo Marita, pakumva kuti Yesu alinkudza, anamuka kukakomana ndi Iye; koma Maria anakhalabe m'nyumba.
Ndipo m'mene anati ichi anachoka naitana Maria mbale wake m'tseri, ndi kuti, Wafika Mphunzitsi, akuitana iwe.