Koma ngakhale tsopano ndidziwa kuti zinthu zilizonse mukapempha Mulungu, adzakupatsani Mulungu.
Yohane 11:23 - Buku Lopatulika Yesu ananena naye, Mlongo wako adzauka. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Yesu ananena naye, Mlongo wako adzauka. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Yesu adamuuza kuti, “Mlongo wako adzauka.” Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Yesu anati kwa iye, “Mlongo wako adzauka.” |
Koma ngakhale tsopano ndidziwa kuti zinthu zilizonse mukapempha Mulungu, adzakupatsani Mulungu.
Yesu ananena naye, Kodi sindinati kwa iwe, kuti, ngati ukhulupirira, udzaona ulemerero wa Mulungu?