ananena, Tulukani, pakuti kabuthuko sikanafe koma kali m'tulo. Ndipo anamseka Iye pwepwete.
Yohane 11:12 - Buku Lopatulika Chifukwa chake ophunzira ake anati kwa Iye, Ambuye, ngati ali m'tulo adzachira. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Chifukwa chake ophunzira ake anati kwa Iye, Ambuye, ngati ali m'tulo adzachira. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Apo ophunzira ake adati, “Ambuye, ngati wagona tulo, achira.” Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ophunzira ake anayankha kuti, “Ambuye, ngati wagona adzapeza bwino.” |
ananena, Tulukani, pakuti kabuthuko sikanafe koma kali m'tulo. Ndipo anamseka Iye pwepwete.
Izi anati, ndipo zitatha izi ananena nao, Lazaro bwenzi lathu ali m'tulo; koma ndimuka kukamuukitsa iye tulo take.