Chifukwa chake ambiri a mwa Ayuda amene anadza kwa Maria, m'mene anaona chimene anachita, anakhulupirira Iye.
Yohane 10:42 - Buku Lopatulika Ndipo ambiri anakhulupirira Iye komweko. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo ambiri anakhulupirira Iye komweko. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Motero anthu ambiri adakhulupirira Yesu kumeneko. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ndipo pamalo amenewo ambiri anakhulupirira Yesu. |
Chifukwa chake ambiri a mwa Ayuda amene anadza kwa Maria, m'mene anaona chimene anachita, anakhulupirira Iye.
Kungakhale kotero, ambiri a mwa akulu anakhulupirira Iye; koma chifukwa cha Afarisi sanavomereze, kuti angaletsedwe m'sunagoge,
Koma pamene anali mu Yerusalemu pa Paska pachikondwerero, ambiri anakhulupirira dzina lake, pakuona zizindikiro zake zimene anachitazi.
Ndipo m'mzinda muja anthu Asamariya ambiri anamkhulupirira Iye chifukwa cha mau a mkazi, wochita umboniyo, kuti, Anandiuza ine zinthu zilizonse ndinazichita.
Koma ambiri a m'khamu la anthu anakhulupirira Iye; ndipo ananena, Pamene Khristu akadza kodi adzachita zizindikiro zambiri zoposa zimene adazichita ameneyo?