Yohane 10:23 - Buku Lopatulika Ndipo Yesu analikuyendayenda mu Kachisi m'khonde la Solomoni. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo Yesu analikuyendayenda m'Kachisi m'khonde la Solomoni. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Yesu ankangodziyendera m'Nyumba ya Mulungu, m'khonde lotchedwa Khonde la Solomoni. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero ndipo Yesu ankayenda mʼbwalo la Nyumbayo ku malo a Solomoni. |
Koma m'mene anagwira Petro ndi Yohane, anawathamangira pamodzi anthu onse kukhonde lotchedwa la Solomoni, alikudabwa ndithu.
Ndipo mwa manja a atumwi zizindikiro ndi zozizwa zambiri zinachitidwa pa anthu; ndipo anali onse ndi mtima umodzi m'khonde la Solomoni.