Wolipidwa amene sakhala mbusa, amene nkhosa sizili zake za yekha, aona mmbulu ulinkudza, nasiya nkhosazo, nathawa; ndipo mmbulu uzikwatula, nuzibalalitsa;
Yohane 10:13 - Buku Lopatulika chifukwa ali wolipidwa, ndipo sasamala nkhosa. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 chifukwa ali wolipidwa, ndipo sasamala nkhosa. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Wolembedwa ntchito uja amathaŵa, chifukwa amangotsata malipiro chabe, ndipo salabadirako za nkhosazo. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Munthuyo amathawa chifukwa ndi wantchito ndipo sasamalira chilichonse cha nkhosazo. |
Wolipidwa amene sakhala mbusa, amene nkhosa sizili zake za yekha, aona mmbulu ulinkudza, nasiya nkhosazo, nathawa; ndipo mmbulu uzikwatula, nuzibalalitsa;
Koma ananena ichi si chifukwa analikusamalira osauka, koma chifukwa anali mbala, ndipo pokhala nalo thumba, amaba zoikidwamo.
Ndipo anamgwira Sostene, mkulu wa sunagoge, nampanda kumpando wachiweruziro. Ndipo Galio sanasamalire zimenezi.
Koma ndifuna kuti mukhale osalabadira. Iye amene wosakwatira alabadira zinthu za Ambuye, kuti akondweretse Ambuye;