Yohane 1:20 - Buku Lopatulika Ndipo anavomera, wosakana; nalola kuti, Sindine Khristu. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo anavomera, wosakana; nalola kuti, Sindine Khristu. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Iye adayankha mosabisa konse, adanenetsa ndithu kuti, “Inetu sindine Mpulumutsi wolonjezedwa uja ai.” Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Iye sanalephere kuvomereza, koma iye anavomereza momasuka kuti, “Ine sindine Khristu.” |
Ndipo pakukwaniritsa njira yake Yohane, ananena, Muyesa kuti ine ndine yani? Ine sindine Iye. Koma taonani, akudza wina wonditsata ine, amene sindiyenera kummasulira nsapato za pa mapazi ake.