Yeremiya 7:1 - Buku Lopatulika Mau amene anadza kwa Yeremiya kuchokera kwa Yehova, kuti, Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Mau amene anadza kwa Yeremiya kuchokera kwa Yehova, kuti, Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Chauta adauza Yeremiya mau aŵa akuti, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Mawu amene Yehova anayankhula kwa Yeremiya ndi awa, |
Mau amene anadza kwa Yeremiya za anthu onse a Yuda chaka chachinai cha Yehoyakimu mwana wake wa Yosiya, mfumu ya Yuda; ndicho chaka choyamba cha Nebukadinezara mfumu ya ku Babiloni;
Ima m'chipata cha nyumba ya Yehova, lalikira m'menemo mau awa, ndi kuti, Tamvani mau a Yehova, inu nonse a Yuda, amene alowa m'zipata izi kuti mugwadire Yehova.