m'menemo mfumu inalola Ayuda okhala mu mzinda uliwonse asonkhane, ndi kulimbikira moyo wao, kuononga, kupha, ndi kupulula mphamvu yonse ya anthu ndi ya dziko yofuna kuwathira nkhondo, iwo, ana ao aang'ono, ndi akazi ao, ndi kulanda zofunkha zao,
Yeremiya 48:4 - Buku Lopatulika Mowabu waonongedwa; ang'ono ake amveketsa kulira. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Mowabu waonongedwa; ang'ono ake amveketsa kulira. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Mowabu waonongeka, ana ake akulira kwambiri. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Mowabu wawonongeka; ana ake angʼonoangʼono akulira kwambiri. |
m'menemo mfumu inalola Ayuda okhala mu mzinda uliwonse asonkhane, ndi kulimbikira moyo wao, kuononga, kupha, ndi kupulula mphamvu yonse ya anthu ndi ya dziko yofuna kuwathira nkhondo, iwo, ana ao aang'ono, ndi akazi ao, ndi kulanda zofunkha zao,
Munthuyo akhale ngati mizinda imene Yehova anapasula, osalekerera; amve mfuu mamawa, ndi mkuwo pausana;
Pakuti adzakwera pa chikweza cha Luhiti ndi kulira kosaleka; pakuti pa chitsiko cha Horonaimu amva kulira kowawa kwa chionongeko.