Ndipo Yehova anati kwa ine, Kodi uona chiyani, Yeremiya? Ndipo ndinati, Nkhuyu, nkhuyu zabwino, nzabwino ndithu; zoipazo nzoipa ndithu, zosadyeka poti nzoipa.
Yeremiya 24:4 - Buku Lopatulika Ndipo mau a Yehova anadza kwa ine, kuti, Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo mau a Yehova anadza kwa ine, kuti, Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Tsono Chauta adandiwuza kuti, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Tsono Yehova anandiwuza kuti, |
Ndipo Yehova anati kwa ine, Kodi uona chiyani, Yeremiya? Ndipo ndinati, Nkhuyu, nkhuyu zabwino, nzabwino ndithu; zoipazo nzoipa ndithu, zosadyeka poti nzoipa.
Chifukwa Yehova, Mulungu wa Israele, atero, Monga nkhuyu zabwino izi, momwemo ndidzasamalira am'nsinga a Yuda, amene ndawachotsera m'malo muno kunka kudziko la Ababiloni, kuwachitira bwino.