amene anamdzera mau a Yehova masiku a Yosiya mwana wake wa Amoni, mfumu ya Ayuda chaka chakhumi ndi chitatu cha ufumu wake.
Yeremiya 16:1 - Buku Lopatulika Ndiponso mau a Yehova anadza kwa ine, kuti, Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndiponso mau a Yehova anadza kwa ine, kuti, Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Chauta adandiwuza kuti, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Kenaka Yehova anandiwuza kuti, |
amene anamdzera mau a Yehova masiku a Yosiya mwana wake wa Amoni, mfumu ya Ayuda chaka chakhumi ndi chitatu cha ufumu wake.
Ndipo ndidzakulanditsa iwe m'dzanja la oipa, ndipo ndidzakuombola iwe m'dzanja la oopsa.