Yeremiya 13:8 - Buku Lopatulika Ndipo mau a Yehova anadza kwa ine, kuti, Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo mau a Yehova anadza kwa ine, kuti, Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Apo mau a adandifikanso: Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Pamenepo Yehova anandiwuza kuti, |
Ndipo ndinanka ku Yufurate, ndikukumba, nditenga mpango m'malo m'mene ndinaubisamo; ndipo, taonani, mpango unaonongeka, wosayenera kanthu.
Yehova atero, Momwemo ndidzaononga kudzitama kwa Yuda, ndi kudzitama kwakukulu kwa Yerusalemu.
Ndipo ndinapenya, ndipo taonani, kuthambo lokhala pamwamba pa mitu ya akerubi kudaoneka ngati mwala wasafiro, ngati maonekedwe a chifaniziro cha mpando wachifumu pamwamba pao.