Yeremiya 13:3 - Buku Lopatulika Ndipo mau a Yehova anadza kwa ine nthawi yachiwiri, kuti, Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo mau a Yehova anadza kwa ine nthawi yachiwiri, kuti, Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Chauta adandiwuzanso mau kachiŵiri kuti, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Kenaka Yehova anandiyankhulanso kachiwiri kuti, |
Tenga mpango umene unaugula, umene uli m'chuuno mwako, nuuke, nupite ku Yufurate, nuubise m'menemo m'phanga la m'mwala.
Yerusalemu, ndi mizinda ya Yuda, ndi mafumu ake omwe, ndi akulu ake, kuwayesa iwo bwinja, chizizwitso, chotsonyetsa, ndi chitemberero; monga lero lino;