Yeremiya 11:1 - Buku Lopatulika Mau amene anadza kwa Yeremiya kuchokera kwa Yehova, kuti, Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Mau amene anadza kwa Yeremiya kuchokera kwa Yehova, kuti, Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Chauta adauza Yeremiya kuti, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Yehova anayankhula ndi Yeremiya kuti, |
Tsanulirani ukali wanu pa amitundu osakudziwani Inu, ndi pa mabanja osaitana dzina lanu; pakuti anadya Yakobo, inde, anamudya namutha, napasula mokhalamo mwake.