Tito 2:9 - Buku Lopatulika Akapolo amvere ambuye ao a iwo okha, nawakondweretse m'zonse; osakana mau ao; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Akapolo amvere ambuye ao a iwo okha, nawakondweretse m'zonse; osakana mau ao; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Antchito azimvera ambuye ao, aziŵakondweretsa pa zonse. Asamatsutsana nawo Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Phunzitsa akapolo kuti azigonjera ambuye awo mu zinthu zonse ndi kuwakondweretsa. Asamatsutsane nawo |