Ndipo taona, Bowazi anafuma ku Betelehemu, nati kwa ocheka, Yehova akhale nanu. Namyankha iwo, Yehova akudalitseni.
Rute 2:5 - Buku Lopatulika Nati Bowazi kwa mnyamata woyang'anira ochekawo, Mkazi uyu ngwa yani? Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Nati Bowazi kwa mnyamata woyang'anira ochekawo, Mkazi uyu ngwa yani? Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Tsono Bowazi adafunsa kapitao wake amene ankayang'anira anthu okolola aja kuti, “Kodi mai uyu ndani?” Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Bowazi anafunsa kapitawo wake amene ankayangʼanira okolola aja kuti, “Mayi uyo ndi ndani?” |
Ndipo taona, Bowazi anafuma ku Betelehemu, nati kwa ocheka, Yehova akhale nanu. Namyankha iwo, Yehova akudalitseni.
Ndipo mnyamata woyang'anira ochekawo anayankha nati, Ndiye mkazi Mmowabuyo anabwera ndi Naomi ku dziko la Mowabu;