ng'ombe yamphongo imodzi, nkhosa yamphongo imodzi, mwanawankhosa mmodzi wa chaka chimodzi, zikhale nsembe yopsereza;
Numeri 7:82 - Buku Lopatulika tonde mmodzi akhale nsembe yauchimo; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 tonde mmodzi akhale nsembe yauchimo; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa tonde mmodzi akhale nsembe yauchimo. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero mbuzi yayimuna imodzi ya nsembe yopepesera machimo; |
ng'ombe yamphongo imodzi, nkhosa yamphongo imodzi, mwanawankhosa mmodzi wa chaka chimodzi, zikhale nsembe yopsereza;
ndi nsembe yoyamika, ng'ombe ziwiri, nkhosa zamphongo zisanu, atonde asanu, anaankhosa asanu a chaka chimodzi; ichi ndi chopereka cha Ahira mwana wa Enani.