Muwatengenso akalonga, kalonga mmodzi ku fuko limodzi, agawe dziko likhale cholowa chao.
Numeri 34:29 - Buku Lopatulika Iwo ndiwo amene Yehova analamulira agawire ana a Israele cholowa chao m'dziko la Kanani. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Iwo ndiwo amene Yehova analamulira agawire ana a Israele cholowa chao m'dziko la Kanani. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Ameneŵa ndiwo amene Chauta adalamula kuti agaŵe choloŵa cha Aisraele m'dziko la Kanani.” Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Awa ndiwo mayina a anthu amene Yehova analamula kuti agawe cholowa cha Aisraeli mʼdziko la Kanaani. |
Muwatengenso akalonga, kalonga mmodzi ku fuko limodzi, agawe dziko likhale cholowa chao.
Izi ndizo zolowa anazigawa Eleazara wansembe, ndi Yoswa mwana wa Nuni, ndi akulu a nyumba za atate a mafuko a ana a Israele, zikhale zaozao, ndi kulota maere ku Silo pamaso pa Yehova ku khomo la chihema chokomanako. Momwemo anatha kuligawa dziko.