Wa fuko la ana a Asere, kalonga Ahihudi mwana wa Selomi.
M'fuko la ana a Asere akhale Ahihudi mwana wa Selomi.
Ahihudi mwana wa Selomi, mtsogoleri wochokera ku fuko la Aseri;
Wa fuko la ana a Isakara, kalonga Palatiele mwana wa Azani.
Wa fuko la ana a Nafutali, kalonga Pedahele mwana wa Amihudi.