Pomwepo Isiboseti anatumiza namchotsera kwa mwamuna wake, kwa Palatiele mwana wa Laisi.
Numeri 34:26 - Buku Lopatulika Wa fuko la ana a Isakara, kalonga Palatiele mwana wa Azani. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Wa fuko la ana a Isakara, kalonga Palatiele mwana wa Azani. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa M'fuko la ana a Isakara akhale Palatiele mwana wa Azani. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Palitieli mwana wa Azani, mtsogoleri wochokera ku fuko la Isakara, |
Pomwepo Isiboseti anatumiza namchotsera kwa mwamuna wake, kwa Palatiele mwana wa Laisi.