Baibulo la pa intaneti

Zotsatsa


Baibulo lonse Chipangano Chakale Chipangano Chatsopano




Numeri 34:25 - Buku Lopatulika

Wa fuko la ana a Zebuloni, kalonga Elizafani mwana wa Paranaki.

Onani mutuwo

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

Wa fuko la ana a Zebuloni, kalonga Elizafani mwana wa Paranaki.

Onani mutuwo

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

M'fuko la ana a Zebuloni akhale Elizafani mwana wa Paranaki.

Onani mutuwo

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

Elizafani mwana wa Parinaki, mtsogoleri wochokera ku fuko la Zebuloni;

Onani mutuwo



Numeri 34:25
2 Mawu Ofanana  

Wa fuko la ana a Efuremu, kalonga Kemuwele mwana wa Sifutani.


Wa fuko la ana a Isakara, kalonga Palatiele mwana wa Azani.