Numeri 34:23 - Buku Lopatulika Wa ana a Yosefe; wa fuko la ana a Manase, kalonga Haniyele mwana wa Efodi. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Wa ana a Yosefe; wa fuko la ana a Manase, kalonga Haniyele mwana wa Efodi. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Mwa ana a Yosefe, m'fuko la ana a Manase akhale Haniyele mwana wa Efodi. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Hanieli mwana wa Efodi, mtsogoleri wochokera ku fuko la Manase, mwana wa Yosefe; |