Wa fuko la ana a Dani, kalonga Buki mwana wa Yogili.
M'fuko la ana a Dani akhale Buki mwana wa Yogili.
Buki mwana wa Yogili, mtsogoleri wochokera ku fuko la Dani;
Ndipo anayandikiza, nati Tidzamangira zoweta zathu makola kuno, ndi ana athu mizinda;
Wa fuko la Benjamini, Elidadi mwana wa Kisiloni.
Wa ana a Yosefe; wa fuko la ana a Manase, kalonga Haniyele mwana wa Efodi.