Benjamini ndiye mmbulu wakulusalusa; m'mamawa adzadya chomotola, madzulo adzagawa zofunkha.
Numeri 34:21 - Buku Lopatulika Wa fuko la Benjamini, Elidadi mwana wa Kisiloni. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Wa fuko la Benjamini, Elidadi mwana wa Kisiloni. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa M'fuko la Benjamini akhale Elidadi mwana wa Kisiloni. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Elidadi mwana wa Kisiloni, wochokera ku fuko la Benjamini; |
Benjamini ndiye mmbulu wakulusalusa; m'mamawa adzadya chomotola, madzulo adzagawa zofunkha.
Apo pali Benjamini wamng'ono, wakuwachita ufumu, akulu a Yuda, ndi a upo wao, akulu a Zebuloni, akulu a Nafutali.
Za Benjamini anati, Wokondedwa wa Yehova adzakhala ndi Iye mokhazikika; am'phimba tsiku lonse, inde akhalitsa pakati pa mapewa ake.