Ndipo anatenganso pakati, nabala mwana wamwamuna nati, Chifukwa anamva Yehova kuti anandida ine, anandipatsa ine mwana wamwamuna uyunso; ndipo anamutcha dzina lake Simeoni.
Numeri 34:20 - Buku Lopatulika Wa fuko la ana a Simeoni, Semuele mwana wa Amihudi. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Wa fuko la ana a Simeoni, Semuele mwana wa Amihudi. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa M'fuko la ana a Simeoni akhale Semuele mwana wa Amihudi. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Semueli mwana wa Amihudi, wochokera ku fuko la Simeoni; |
Ndipo anatenganso pakati, nabala mwana wamwamuna nati, Chifukwa anamva Yehova kuti anandida ine, anandipatsa ine mwana wamwamuna uyunso; ndipo anamutcha dzina lake Simeoni.
Ndi kumalire a Benjamini, kuyambira mbali ya kum'mawa kufikira mbali ya kumadzulo; Simeoni, gawo limodzi.