Numeri 33:44 - Buku Lopatulika Nachokera ku Oboti, nayenda namanga mu Iyeabarimu, m'malire a Mowabu. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Nachokera ku Oboti, nayenda namanga m'Iyeabarimu, m'malire a Mowabu. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Adanyamuka ku Oboti, nakamanga mahema ao ku Iyeabarimu, m'dziko la Mowabu. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Atachoka ku Oboti anakamanga ku Iye-Abarimu. |
Ndipo anachoka ku Oboti, namanga mahema ku Iyeabarimu, m'chipululu chakuno cha Mowabu, kotulukira dzuwa.