Nachokera ku Punoni, nayenda namanga mu Oboti.
Nachokera ku Punoni, nayenda namanga m'Oboti.
Adanyamuka ku Punoni, nakamanga mahema ao ku Oboti.
Atachoka ku Punoni anakamanga ku Oboti.
Pamenepo ana a Israele anayenda ulendo, namanga mahema mu Oboti.
Ndipo anachoka ku Oboti, namanga mahema ku Iyeabarimu, m'chipululu chakuno cha Mowabu, kotulukira dzuwa.
Nachokera ku Zalimona, nayenda namanga mu Punoni.
Nachokera ku Oboti, nayenda namanga mu Iyeabarimu, m'malire a Mowabu.