Numeri 33:40 - Buku Lopatulika Ndipo Mkanani, mfumu ya Aradi, wakukhala kumwera m'dziko la Kanani, anamva za kudza kwao kwa ana a Israele. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo Mkanani, mfumu ya Aradi, wakukhala kumwera m'dziko la Kanani, anamva za kudza kwao kwa ana a Israele. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Mfumu ya ku Aradi, Mkanani amene ankakhala m'dziko la Kanani, adamva kuti Aisraele akubwera. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Mfumu ya Akanaani ya ku Aradi yomwe inkakhala ku Negevi kummwera kwa Kanaani, inamva kuti Aisraeli akubwera. |
Ndipo Aroni ndiye wa zaka zana limodzi mphambu makumi awiri kudza zitatu pakufa iye m'phiri la Hori.