Numeri 33:32 - Buku Lopatulika Nachokera ku Bene-Yaakani, nayenda namanga mu Hori Hagidigadi. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Nachokera ku Bene-Yaakani, nayenda namanga m'Hori Hagidigadi. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Adanyamuka ku Beneyakana, nakamanga mahema ao ku Horo-Hagidigadi. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Atachoka ku Beni Yaakani anakamanga ku Hori-Hagidigadi. |
Ndipo ana a Israele anayenda ulendo wao kuchokera ku zitsime za ana a Yaakani kufikira ku Mosera. Kumeneko anamwalira Aroni, ndi kumeneko anamuika; ndipo Eleazara mwana wake anachita ntchito ya nsembe m'malo mwake.
Kuchokerako ananka ulendo ku Gudigoda, ndi kuchokera ku Gudigoda kunka ku Yotibata, dziko la mitsinje yamadzi.