Ndipo Mose anavula Aroni zovala zake, naveka Eleazara mwana wake; ndipo Aroni anafa pomwepo pamwamba paphiri. Pamenepo Mose ndi Eleazara anatsika m'phirimo.
Numeri 33:30 - Buku Lopatulika Nachokera ku Hasimona, nayenda namanga mu Meseroti. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Nachokera ku Hasimona, nayenda namanga m'Meseroti. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Adanyamuka ku Hasimona, nakamanga mahema ao ku Meseroti. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Atachoka ku Hasimona anakamanga ku Moseroti. |
Ndipo Mose anavula Aroni zovala zake, naveka Eleazara mwana wake; ndipo Aroni anafa pomwepo pamwamba paphiri. Pamenepo Mose ndi Eleazara anatsika m'phirimo.
nufe m'phiri m'mene ukweramo, nuitanidwe kunka kwa anthu a mtundu wako; monga Aroni mbale wako anafa m'phiri la Hori, naitanidwa kunka kwa anthu a mtundu wake;