Nachokera ku Makeloti, nayenda namanga mu Tahata.
Nachokera ku Makeloti, nayenda namanga m'Tahata.
Adanyamuka ku Makeloti, nakamanga mahema ao ku Tahati.
Atachoka ku Mekheloti anakamanga ku Tahati.
Nachokera ku Harada, nayenda namanga mu Makeloti.
Nachokera ku Tahata, nayenda namanga mu Tera.