Nachokera ku Kehelata, nayenda namanga m'phiri la Sefera.
Adanyamuka ku Kehelata, nakamanga mahema ao ku phiri la Sefera.
Atachoka ku Kehelata anakamanga ku phiri la Seferi.
Nachokera Risa, nayenda namanga mu Kehelata.
Nachokera kuphiri la Sefera, nayenda namanga mu Harada.