Numeri 33:21 - Buku Lopatulika Nachokera ku Libina, nayenda namanga mu Risa. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Nachokera ku Libina, nayenda namanga m'Risa. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Adanyamuka ku Libina, nakamanga mahema ao ku Risa. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Atachoka ku Libina anakamanga ku Risa. |
Awa ndi mau amene Mose ananena kwa Israele wonse, tsidya la Yordani m'chipululu, m'chidikha cha pandunji pa Sufu, pakati pa Parani, ndi Tofele, ndi Labani, ndi Hazeroti, ndi Dizahabu.