Ndipo kazembeyo anabwerera, napeza mfumu ya Asiriya ilikuponyana nkhondo ndi Libina; pakuti anamva kuti inachoka ku Lakisi.
Numeri 33:20 - Buku Lopatulika Nachokera ku Rimoni-Perezi, nayenda namanga mu Libina. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Nachokera ku Rimoni-Perezi, nayenda namanga m'Libina. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Adanyamuka ku Rimoni-Perezi, nakamanga mahema ao ku Libina. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Atachoka ku Rimoni-Perezi anakamanga ku Libina. |
Ndipo kazembeyo anabwerera, napeza mfumu ya Asiriya ilikuponyana nkhondo ndi Libina; pakuti anamva kuti inachoka ku Lakisi.
Ndipo Mose anawatuma a fuko limodzi chikwi chimodzi, kunkhondo, iwowa ndi Finehasi mwana wa Eleazara wansembe, kunkhondo, ndi zipangizo zopatulika, ndi malipenga oliza m'dzanja lake.
Awa ndi mau amene Mose ananena kwa Israele wonse, tsidya la Yordani m'chipululu, m'chidikha cha pandunji pa Sufu, pakati pa Parani, ndi Tofele, ndi Labani, ndi Hazeroti, ndi Dizahabu.
Pamenepo Yoswa ndi Aisraele onse naye anapitirira kuchokera ku Makeda kunka ku Libina, nathira nkhondo pa Libina;