Nachokera ku Ritima, nayenda namanga mu Rimoni-Perezi.
Nachokera ku Ritima, nayenda namanga m'Rimoni-Perezi.
Adanyamuka ku Ritima, nakamanga mahema ao ku Rimoni-Perezi.
Atachoka ku Ritima anakamanga ku Rimoni-Perezi.
Nachokera ku Hazeroti, nayenda namanga mu Ritima.
Nachokera ku Rimoni-Perezi, nayenda namanga mu Libina.
Aini, Rimoni ndi Eteri ndi Asani; mizinda inai ndi midzi yao;