Ndipo atatero anthuwo ananka ulendo wao kuchokera ku Hazeroti, namanga mahema ao m'chipululu cha Parani.
Numeri 33:18 - Buku Lopatulika Nachokera ku Hazeroti, nayenda namanga mu Ritima. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Nachokera ku Hazeroti, nayenda namanga m'Ritima. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Adanyamuka ku Hazeroti, nakamanga mahema ao ku Ritima. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Atachoka ku Heziroti anakamanga ku Ritima. |
Ndipo atatero anthuwo ananka ulendo wao kuchokera ku Hazeroti, namanga mahema ao m'chipululu cha Parani.