Nachokera ku Kibroti-Hatava, nayenda namanga mu Hazeroti.
Nachokera ku Kibroti-Hatava, nayenda namanga m'Hazeroti.
Adanyamuka ku Kibroti-Hatava, nakamanga mahema ao ku Haseroti.
Atachoka ku Kiburoti-Hataava anakamanga misasa yawo ku Heziroti.
Ndipo anatcha malowo dzina lake Kibroti-Hatava; popeza pamenepo anaika anthu osusuka.
Kuchokera ku Kibroti-Hatava anthuwo anayenda kunka ku Hazeroti; nakhala ku Hazeroti.
Nachokera ku Hazeroti, nayenda namanga mu Ritima.