Nachokera ku Dofika, nayenda namanga mu Alusi.
Nachokera ku Dofika, nayenda namanga m'Alusi.
Adanyamuka ku Dofika, nakamanga mahema ao ku Alusi.
Atachoka ku Dofika anakamanga misasa yawo ku Alusi.
Nachokera ku chipululu cha Sini, nayenda namanga mu Dofika.
Nachokera ku Alusi, nayenda namanga mu Refidimu; kumeneko kunalibe madzi kuti anthu amwe.