Ndipo anachoka ku Elimu, ndi khamu lonse la ana a Israele linalowa m'chipululu cha Sini, ndicho pakati pa Elimu ndi Sinai, tsiku lakhumi ndi chisanu la mwezi wachiwiri atatuluka m'dziko la Ejipito.
Numeri 33:11 - Buku Lopatulika Nachokera ku Nyanja Yofiira, nayenda namanga m'chipululu cha Sini. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Nachokera ku Nyanja Yofiira, nayenda namanga m'chipululu cha Sini. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Adanyamuka ku Nyanja Yofiira, nakamanga mahema ao ku chipululu cha Sini. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Atachoka ku Nyanja Yofiira anakamanga misasa yawo mʼchipululu cha Sini. |
Ndipo anachoka ku Elimu, ndi khamu lonse la ana a Israele linalowa m'chipululu cha Sini, ndicho pakati pa Elimu ndi Sinai, tsiku lakhumi ndi chisanu la mwezi wachiwiri atatuluka m'dziko la Ejipito.