Numeri 32:24 - Buku Lopatulika Dzimangireni mizinda ya ana anu, ndi makola a zoweta zanu; ndipo muzichite zotuluka m'kamwa mwanu. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Dzimangireni midzi ya ana anu, ndi makola a zoweta zanu; ndipo muzichite zotuluka m'kamwa mwanu. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Mangani mizinda ya ana anu, ndi makola a nkhosa zanu, koma muchitedi zimene mwalonjeza.” Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Amangireni akazi ndi ana anu mizinda, mangani makola a ziweto zanu, koma chitani zomwe mwalonjeza.” |
Munthu akachitira Yehova chowinda, kapena akalumbira lumbiro ndi kumangira moyo wake chodziletsa, asaipse mau ake; azichita monga mwa zonse zotuluka m'kamwa mwake.
Ndipo ana a Gadi ndi ana a Rubeni ananena ndi Mose, nati, Anyamata anu adzachita monga mbuyanga alamulira.