Ndipo ng'ombe zidafikira zikwi makumi atatu mphambu zisanu ndi chimodzi; pamenepo msonkho wa Yehova ndiwo makumi asanu ndi awiri mphambu ziwiri.
Numeri 31:39 - Buku Lopatulika Ndipo abulu anafikira zikwi makumi atatu ndi mazana asanu; pamenepo msonkho wa Yehova ndiwo makumi asanu ndi limodzi mphambu mmodzi. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo abulu anafikira zikwi makumi atatu ndi mazana asanu; pamenepo msonkho wa Yehova ndiwo makumi asanu ndi limodzi mphambu mmodzi. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Abulu analipo 30,500, ndipo 61 anali gawo la Chauta. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero abulu analipo 30,500 ndipo gawo la Yehova linali 61; |
Ndipo ng'ombe zidafikira zikwi makumi atatu mphambu zisanu ndi chimodzi; pamenepo msonkho wa Yehova ndiwo makumi asanu ndi awiri mphambu ziwiri.
Ndipo anthu anafikira zikwi khumi ndi zisanu ndi chimodzi; pamenepo msonkho wa Yehova ndiwo anthu makumi atatu mphambu awiri.